Saturday, November 20, 2010

Khoswe ndi mphemvu.

Do animals ever smack their young one? Like discipline them?
Nanga ndi chifukwa chani khoswe alibe khalidwe?
Makoswe nonse omwe muli ndi ana, chonde yesetsani kupatsa ana anuwo mwambo. Ife anthu tatopa ndi makhalidwe anu oyipa, okuba!
Ena ndi Ana a mphemvu..... Khalidwe labwino linawadutsa.

I wonder what would happen if a mphemvu was to marry a khoswe?
Dziko lingayipe ndithu!

No comments:

Post a Comment