Wednesday, September 23, 2009

Khoswe wachitsamunda.

Nkhaniyi ikupitirira kuchokera ku yahoo bulogi (pepani koma yahoo ndi blog zilibe Chichewa chake).
Monga ndinalongosolera, makoswe amwa mowa wa a munanga. Panopa nyumba yonse ili gwedegwede, makoswe aledzera, chisangalalo chodzadza tsaya, amunanga ali msunamu kuno.
Makoswe agenda kupolisi ndi nthangala za chamba. Kuba mowa?
Sindikudziwa.............

***nkhaniyi ndi yeniyeni**

No comments:

Post a Comment